Genesis 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ili ndi buku la mbiri ya Adamu. Pa tsiku* limene Mulungu analenga Adamu, anamupanga mʼchifaniziro cha Mulungu.+
5 Ili ndi buku la mbiri ya Adamu. Pa tsiku* limene Mulungu analenga Adamu, anamupanga mʼchifaniziro cha Mulungu.+