Genesis 36:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Mfumu Disoni, Mfumu Ezeri ndi Mfumu Disani.+ Amenewa ndi amene anali mafumu a fuko la Ahori mogwirizana ndi ufumu wawo mʼdziko la Seiri.
30 Mfumu Disoni, Mfumu Ezeri ndi Mfumu Disani.+ Amenewa ndi amene anali mafumu a fuko la Ahori mogwirizana ndi ufumu wawo mʼdziko la Seiri.