Genesis 37:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Isiraeli ankamukonda kwambiri Yosefe kuposa ana ake onse,+ chifukwa anali mwana amene anamʼbereka atakalamba. Choncho anamusoketsera mkanjo wokongola. Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 37:3 Nsanja ya Olonda,8/1/2014, tsa. 12
3 Isiraeli ankamukonda kwambiri Yosefe kuposa ana ake onse,+ chifukwa anali mwana amene anamʼbereka atakalamba. Choncho anamusoketsera mkanjo wokongola.