-
Genesis 37:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Kenako Isiraeli anauza Yosefe kuti: “Kodi abale ako sakudyetsa ziweto pafupi ndi ku Sekemu? Tabwera ndikutume kwa iwo.” Iye anati: “Chabwino bambo.”
-