Genesis 37:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Rubeni+ atamva zimenezo anayesa kumupulumutsa. Iye anati: “Ayi, tisamuphe.”+