Genesis 37:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Tiyeni timugulitse+ kwa Aisimaeliwa, tisamuvulaze. Ndipotu ndi mʼbale wathu ameneyu, magazi amodzi.”* Choncho iwo anamvera zimene mʼbale wawoyo ananena. Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 37:27 Nsanja ya Olonda,7/15/1992, tsa. 4
27 Tiyeni timugulitse+ kwa Aisimaeliwa, tisamuvulaze. Ndipotu ndi mʼbale wathu ameneyu, magazi amodzi.”* Choncho iwo anamvera zimene mʼbale wawoyo ananena.