Genesis 37:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Kenako, iwo anatumiza mkanjo uja kwa bambo awo ndipo bambowo anauzidwa kuti: “Tapeza mkanjo uwu. Chonde, uonetsetseni kuti muone ngati uli mkanjo wa mwana wanu kapena ayi.”+
32 Kenako, iwo anatumiza mkanjo uja kwa bambo awo ndipo bambowo anauzidwa kuti: “Tapeza mkanjo uwu. Chonde, uonetsetseni kuti muone ngati uli mkanjo wa mwana wanu kapena ayi.”+