Genesis 37:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Ana ake onse aamuna ndi aakazi ankapita kukamutonthoza, koma iye ankakana kutonthozedwa. Ankanena kuti: “Ayi! Ndidzalira mpaka kutsikira ku Manda*+ kumene kuli mwana wanga.” Ndipo bambo akewo anapitiriza kumulira. Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 37:35 Nsanja ya Olonda,6/1/1995, tsa. 7 Kukhala ndi Moyo Kosatha, ptsa. 82-83
35 Ana ake onse aamuna ndi aakazi ankapita kukamutonthoza, koma iye ankakana kutonthozedwa. Ankanena kuti: “Ayi! Ndidzalira mpaka kutsikira ku Manda*+ kumene kuli mwana wanga.” Ndipo bambo akewo anapitiriza kumulira.