-
Genesis 38:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
38 Pa nthawi imeneyi, Yuda anasiyana ndi abale ake, ndipo anakamanga tenti yake pafupi ndi munthu wina wa Chiadulamu, dzina lake Hira.
-