Genesis 38:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Patapita nthawi, Yuda anatengera mkazi Ere, mwana wake woyamba. Mkaziyo dzina lake anali Tamara.+