-
Genesis 38:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Yuda anauza Tamara mpongozi wake kuti: “Pita kunyumba kwa bambo ako, ukakhale kumeneko monga mkazi wamasiye kufikira Shela mwana wanga wamwamuna atakula.” Anatero chifukwa mumtima mwake anati: “Nayenso Shela angamwalire ngati abale ake aja.”+ Choncho Tamara anapita kukakhala kunyumba kwa bambo ake.
-