Genesis 38:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Patapita nthawi, mkazi wa Yuda, yemwe anali mwana wa Sua,+ anamwalira. Nthawi yolira maliro itatha Yuda anapita ku Timuna,+ kumene anyamata ake ankameta ubweya wa nkhosa zake. Anapita ndi mnzake Hira wa Chiadulamu uja.+
12 Patapita nthawi, mkazi wa Yuda, yemwe anali mwana wa Sua,+ anamwalira. Nthawi yolira maliro itatha Yuda anapita ku Timuna,+ kumene anyamata ake ankameta ubweya wa nkhosa zake. Anapita ndi mnzake Hira wa Chiadulamu uja.+