-
Genesis 38:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Tamara atamva zimenezo, anavula zovala zake zaumasiye nʼkufunda nsalu. Kenako anaphimba nkhope yake ndi nsalu ina. Atatero anakakhala pansi pachipata cha Enaimu mʼmbali mwa msewu wopita ku Timuna. Tamara anachita zimenezi poona kuti Shela wakula, koma apongozi ake sakudzamutenga kuti akakhale mkazi wa Shelayo.+
-