Genesis 38:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho Yuda anapatuka nʼkupita pamene panali mkaziyo mʼmbali mwa msewu nʼkumuuza kuti: “Ndikufuna ndigone nawe.” Anamuuza zimenezi chifukwa sankadziwa kuti anali mpongozi wake.+ Koma mkaziyo anayankha kuti: “Mundipatsa chiyani kuti mugone nane?” Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 38:16 Nsanja ya Olonda,1/15/2004, tsa. 30
16 Choncho Yuda anapatuka nʼkupita pamene panali mkaziyo mʼmbali mwa msewu nʼkumuuza kuti: “Ndikufuna ndigone nawe.” Anamuuza zimenezi chifukwa sankadziwa kuti anali mpongozi wake.+ Koma mkaziyo anayankha kuti: “Mundipatsa chiyani kuti mugone nane?”