Genesis 38:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Patapita miyezi itatu, Yuda anauzidwa kuti: “Tamara mpongozi wako wayamba uhule, ndipo ndi woyembekezera.” Yuda atamva zimenezo anati: “Mutulutseni ndipo mumuphe kenako mumuotche.”+
24 Patapita miyezi itatu, Yuda anauzidwa kuti: “Tamara mpongozi wako wayamba uhule, ndipo ndi woyembekezera.” Yuda atamva zimenezo anati: “Mutulutseni ndipo mumuphe kenako mumuotche.”+