Genesis 38:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Pamene ankamutulutsa, Tamarayo anatumiza uthenga kwa apongozi ake kuti: “Mwiniwake wa zinthu izi ndi amene anandipatsa mimbayi.” Ananenanso kuti: “Chonde ziyangʼanitsitseni, muone kuti mpheteyo ndi chingwe chake komanso ndodoyo nʼzandani.”+
25 Pamene ankamutulutsa, Tamarayo anatumiza uthenga kwa apongozi ake kuti: “Mwiniwake wa zinthu izi ndi amene anandipatsa mimbayi.” Ananenanso kuti: “Chonde ziyangʼanitsitseni, muone kuti mpheteyo ndi chingwe chake komanso ndodoyo nʼzandani.”+