Genesis 38:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Koma mwanayo anabweza dzanja lake. Nthawi yomweyo mchimwene wake anatuluka, moti mzambayo anafuula kuti: “Bwanji ukuchita kungʼamba njira?” Nʼchifukwa chake anamupatsa dzina lakuti Perezi.*+
29 Koma mwanayo anabweza dzanja lake. Nthawi yomweyo mchimwene wake anatuluka, moti mzambayo anafuula kuti: “Bwanji ukuchita kungʼamba njira?” Nʼchifukwa chake anamupatsa dzina lakuti Perezi.*+