Genesis 39:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Kenako Aisimaeli+ aja anapita naye Yosefe ku Iguputo+ ndipo anakamugulitsa kwa munthu wina wa ku Iguputo dzina lake Potifara.+ Potifara anali nduna yapanyumba ya Farao, komanso mkulu wa asilikali olondera mfumu. Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 39:1 Nsanja ya Olonda,11/1/2014, ptsa. 12-13
39 Kenako Aisimaeli+ aja anapita naye Yosefe ku Iguputo+ ndipo anakamugulitsa kwa munthu wina wa ku Iguputo dzina lake Potifara.+ Potifara anali nduna yapanyumba ya Farao, komanso mkulu wa asilikali olondera mfumu.