-
Genesis 39:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Mbuye wakeyo anaona kuti Yehova anali ndi mnyamatayo komanso kuti Yehova ankathandiza mnyamatayo kuti chilichonse chimene ankachita chiziyenda bwino.
-