5 Kuyambira pamene Potifara anasankha Yosefe kukhala woyangʼanira nyumba yake ndi zinthu zake zonse, Yehova anapitiriza kudalitsa nyumba ya munthu wa ku Iguputoyo chifukwa cha Yosefe. Yehova anadalitsa zonse zamʼnyumba ya Potifara ndi zakumunda zomwe.+