-
Genesis 39:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Kenako, mkazi wa mbuye wake anayamba kuyangʼana Yosefe momusirira, moti ankamuuza kuti: “Ugone nane.”