-
Genesis 39:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Mkaziyo ankalankhula ndi Yosefe tsiku ndi tsiku, koma iye sanamvere zoti agone pambali pake kapena kuti agone naye.
-