-
Genesis 39:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Choncho mkaziyo anagwira malaya a mnyamatayo nʼkumuuza kuti: “Ugone nane basi!” Koma mnyamatayo anangovula malayawo nʼkuwasiya mʼmanja mwa mkaziyo nʼkuthawira panja.
-