-
Genesis 39:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Mwamuna wake atafika, mkaziyo anamuuzanso mawu omwe aja akuti: “Wantchito wa Chiheberi amene munatibweretsera uja, anabwera kwa ine kuti andichite zachipongwe.
-