Genesis 39:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Zitatero, mbuye wake wa Yosefe anamutenga nʼkukamusiya kundende ya akaidi a mfumu kuti akamutsekere, ndipo Yosefe anakhala kumeneko.+ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 39:20 Nsanja ya Olonda,11/1/2014, ptsa. 14-15
20 Zitatero, mbuye wake wa Yosefe anamutenga nʼkukamusiya kundende ya akaidi a mfumu kuti akamutsekere, ndipo Yosefe anakhala kumeneko.+