-
Genesis 40:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Usiku wina, woperekera zakumwa kwa mfumu ya Iguputo komanso wophika mkate, omwe anali mʼndende aja, aliyense analota maloto ndipo malotowo anali ndi matanthauzo osiyana.
-