-
Genesis 40:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Choncho mkulu wa operekera zakumwa anafotokozera Yosefe maloto ake kuti: “Mʼmaloto anga, ndinaona mtengo wa mpesa uli patsogolo panga.
-