Genesis 40:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pakapita masiku atatu, Farao akutulutsa.* Adzakubwezera ndithu pa ntchito yako yakale,+ yoperekera zakumwa kwa mfumu ngati mmene unkachitira poyamba.+
13 Pakapita masiku atatu, Farao akutulutsa.* Adzakubwezera ndithu pa ntchito yako yakale,+ yoperekera zakumwa kwa mfumu ngati mmene unkachitira poyamba.+