Genesis 40:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pakapita masiku atatu, Farao akutulutsa nʼkukudula mutu.* Adzakupachika pamtengo, ndipo mbalame zidzadya nyama yako.”+
19 Pakapita masiku atatu, Farao akutulutsa nʼkukudula mutu.* Adzakupachika pamtengo, ndipo mbalame zidzadya nyama yako.”+