Genesis 40:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Tsiku lachitatulo linali tsiku lokumbukira kubadwa+ kwa Farao. Mfumuyo inakonzera phwando antchito ake onse. Pa tsikuli, Farao anatulutsa mʼndende* mkulu wa operekera zakumwa ndi mkulu wa ophika mkate, nʼkuwaimiritsa pamaso pa antchito ake onse. Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 40:20 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 44 Nsanja ya Olonda,10/15/1998, tsa. 31
20 Tsiku lachitatulo linali tsiku lokumbukira kubadwa+ kwa Farao. Mfumuyo inakonzera phwando antchito ake onse. Pa tsikuli, Farao anatulutsa mʼndende* mkulu wa operekera zakumwa ndi mkulu wa ophika mkate, nʼkuwaimiritsa pamaso pa antchito ake onse.