-
Genesis 41:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Pambuyo pake anaonanso ngʼombe zina 7 zikutuluka mumtsinje wa Nailowo. Zimenezi zinali zonyansa ndi zowonda, ndipo zinaima pambali pa zonenepazo mʼmbali mwa mtsinjewo.
-