-
Genesis 41:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Ndiye ngʼombe zonyansa ndi zowondazo zinayamba kudya ngʼombe 7 zooneka bwino ndi zonenepa zija. Kenako Farao anadzidzimuka.
-