-
Genesis 41:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Ngala zonyalazo zinayamba kumeza ngala 7 zokhwima ndi zazikulu bwinozo. Kenako Farao anadzidzimuka ndipo anazindikira kuti anali maloto.
-