Genesis 41:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiyeno Farao anauza Yosefe kuti: “Ine ndalota maloto, ndipo palibe munthu amene wakwanitsa kuwamasulira. Koma ndamva kuti iweyo ukamva maloto umatha kumasulira.”+
15 Ndiyeno Farao anauza Yosefe kuti: “Ine ndalota maloto, ndipo palibe munthu amene wakwanitsa kuwamasulira. Koma ndamva kuti iweyo ukamva maloto umatha kumasulira.”+