Genesis 41:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiyeno ndinaona ngʼombe 7 zonenepa ndi zooneka bwino zikutuluka mumtsinje wa Nailo, ndipo zinayamba kudya udzu wa mʼmbali mwa mtsinjewo.+
18 Ndiyeno ndinaona ngʼombe 7 zonenepa ndi zooneka bwino zikutuluka mumtsinje wa Nailo, ndipo zinayamba kudya udzu wa mʼmbali mwa mtsinjewo.+