-
Genesis 41:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Pambuyo pake ndinaonanso ngʼombe zina 7 zikutuluka mumtsinjewo. Ngʼombe zimenezi zinali zonyansa ndi zowonda. Sindinaonepo ngʼombe zonyansa ngati zimenezo mʼdziko lonse la Iguputo.
-