Genesis 41:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Koma pambuyo pa zaka zimenezo, padzabwera zaka 7 za njala. Chakudya chonse chochuluka cha mʼdziko la Iguputo chija chidzaiwalika, ndipo njalayo idzawononga dziko lonse.+
30 Koma pambuyo pa zaka zimenezo, padzabwera zaka 7 za njala. Chakudya chonse chochuluka cha mʼdziko la Iguputo chija chidzaiwalika, ndipo njalayo idzawononga dziko lonse.+