Genesis 41:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Inu Farao muike anthu oyangʼanira mʼdziko lino, ndipo muzitenga gawo limodzi mwa magawo 5 a chakudya cha dziko la Iguputo pa zaka 7 zimene kudzakhale zokolola zochuluka.+
34 Inu Farao muike anthu oyangʼanira mʼdziko lino, ndipo muzitenga gawo limodzi mwa magawo 5 a chakudya cha dziko la Iguputo pa zaka 7 zimene kudzakhale zokolola zochuluka.+