Genesis 41:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Mʼzaka zimene kudzakhale chakudya chambiri, oyangʼanirawo azidzasonkhanitsa tirigu yense nʼkumusunga bwino mʼmizinda ndipo adzakhale wa inu Farao.+
35 Mʼzaka zimene kudzakhale chakudya chambiri, oyangʼanirawo azidzasonkhanitsa tirigu yense nʼkumusunga bwino mʼmizinda ndipo adzakhale wa inu Farao.+