Genesis 41:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Farao anauzanso Yosefe kuti: “Tsopano ndikukuika kukhala woyangʼanira dziko lonse la Iguputo.”+