-
Genesis 41:42Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
42 Atatero, Farao anavula mphete yake yachifumu kudzanja lake nʼkuveka Yosefe. Anamuvekanso zovala zokongola komanso tcheni chagolide mʼkhosi mwake.
-