Genesis 41:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Ndiponso anamukweza pagaleta lina la Farao,* ndipo anthu ankafuula patsogolo pake kuti, “A·vrékh!”* Choncho Farao anamupatsa udindo woyangʼanira dziko lonse la Iguputo.
43 Ndiponso anamukweza pagaleta lina la Farao,* ndipo anthu ankafuula patsogolo pake kuti, “A·vrékh!”* Choncho Farao anamupatsa udindo woyangʼanira dziko lonse la Iguputo.