-
Genesis 41:49Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
49 Yosefe anapitiriza kusunga tirigu, mpaka anachuluka kwambiri ngati mchenga wakunyanja moti anasiya kumuyeza chifukwa sakanathanso kumuyeza chifukwa anali wambiri.
-