Genesis 41:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Mwana woyambayo, Yosefe anamupatsa dzina lakuti Manase*+ chifukwa anati, “Mulungu wandiiwalitsa mavuto anga onse ndi nyumba yonse ya bambo anga.” Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 41:51 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),10/2018, tsa. 28 Nsanja ya Olonda,5/1/2015, tsa. 12
51 Mwana woyambayo, Yosefe anamupatsa dzina lakuti Manase*+ chifukwa anati, “Mulungu wandiiwalitsa mavuto anga onse ndi nyumba yonse ya bambo anga.”