Genesis 41:53 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 53 Kenako zaka 7 zimene mʼdziko la Iguputo munali chakudya chochuluka zinatha.+