Genesis 41:54 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 54 Ndipo zaka 7 za njala zinayamba, mogwirizana ndi zimene Yosefe ananena.+ Njalayo inali mʼmayiko onse, koma dziko lonse la Iguputo linali ndi chakudya.+
54 Ndipo zaka 7 za njala zinayamba, mogwirizana ndi zimene Yosefe ananena.+ Njalayo inali mʼmayiko onse, koma dziko lonse la Iguputo linali ndi chakudya.+