Genesis 41:55 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 55 Kenako njala ija inafika mʼdziko lonse la Iguputo, ndipo anthu anayamba kulirira Farao kuti awapatse chakudya.+ Koma Farao anauza Aiguputo onse kuti: “Pitani kwa Yosefe, ndipo mukachite chilichonse chimene akakuuzeni.”+ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 41:55 Nsanja ya Olonda,5/1/1987, ptsa. 15, 19
55 Kenako njala ija inafika mʼdziko lonse la Iguputo, ndipo anthu anayamba kulirira Farao kuti awapatse chakudya.+ Koma Farao anauza Aiguputo onse kuti: “Pitani kwa Yosefe, ndipo mukachite chilichonse chimene akakuuzeni.”+