Genesis 41:57 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 57 Komanso, anthu padziko lonse lapansi anayamba kubwera ku Iguputo kudzagula chakudya kwa Yosefe, chifukwa njalayo inali itafika poipa kwambiri padziko lonse lapansi.+
57 Komanso, anthu padziko lonse lapansi anayamba kubwera ku Iguputo kudzagula chakudya kwa Yosefe, chifukwa njalayo inali itafika poipa kwambiri padziko lonse lapansi.+