Genesis 42:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Yakobo atamva kuti ku Iguputo kuli tirigu,+ anafunsa ana ake kuti: “Kodi muzingoyangʼanana?”