Genesis 42:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno ana a Isiraeliwo anafika ku Iguputo limodzi ndi anthu ena okagula tirigu, chifukwa mʼdziko la Kanani munali njala.+
5 Ndiyeno ana a Isiraeliwo anafika ku Iguputo limodzi ndi anthu ena okagula tirigu, chifukwa mʼdziko la Kanani munali njala.+